lowezani mabuku a m’baibulo—gawo 1 · ezara anathandiza kuti anthu ayambenso kulambirayehova...
TRANSCRIPT
![Page 1: Lowezani Mabuku a M’Baibulo—Gawo 1 · Ezara Anathandiza kuti anthu ayambenso kulambiraYehova Nehemiya Anathandiza kuti mzinda ndi mpanda wake zimangidwenso KHALANI BWENZI LAYEHOVA](https://reader036.vdocuments.pub/reader036/viewer/2022071010/5fc85387fa69e7034b5c44c9/html5/thumbnails/1.jpg)
Lowezani Mabuku a M’Baibulo—Gawo 1Dulani makadiwa kuti akuthandizeni kuloweza mabuku ena a m’Baibulo a Malemba aChiheberi. Funsani anthu a m’banja mwanu komanso anzanu.
GenesisBuku lofotokoza
mmene paradaiso anathera
EkisodoMulungu anapulumutsaanthu ake modabwitsa
LevitikoMalamulo a Mulungu
anawathandiza kukhalaoyera tsiku lililonse
NumeriEna analephera kukalowa
m’Dziko Lolonjezedwa
KHALANI BWENZI LA YEHOVA � ZOCHITA
s
PINDANI
PINDANI
www.jw.org � 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of PennsylvaniaTsamba 1
![Page 2: Lowezani Mabuku a M’Baibulo—Gawo 1 · Ezara Anathandiza kuti anthu ayambenso kulambiraYehova Nehemiya Anathandiza kuti mzinda ndi mpanda wake zimangidwenso KHALANI BWENZI LAYEHOVA](https://reader036.vdocuments.pub/reader036/viewer/2022071010/5fc85387fa69e7034b5c44c9/html5/thumbnails/2.jpg)
DeuteronomoAnalimbikitsidwa
kuti akhale omvera
YoswaBanja lililonse
linali ndi malo awoawo
OweruzaAnthu a Mulungu
ankachita zinthu zodabwitsa
RuteAnapeza mwamunandiponso pokhala
KHALANI BWENZI LA YEHOVA � ZOCHITA
s
PINDANI
PINDANI
www.jw.org � 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of PennsylvaniaTsamba 2
![Page 3: Lowezani Mabuku a M’Baibulo—Gawo 1 · Ezara Anathandiza kuti anthu ayambenso kulambiraYehova Nehemiya Anathandiza kuti mzinda ndi mpanda wake zimangidwenso KHALANI BWENZI LAYEHOVA](https://reader036.vdocuments.pub/reader036/viewer/2022071010/5fc85387fa69e7034b5c44c9/html5/thumbnails/3.jpg)
1 SamueliMulungu anasankha
Davide kuti akhale mfumu
2 SamueliM’banja lake munali mavutochifukwa cha machimo ake
1 MafumuUfumu unagawanika,
wina kumpoto wina kumwera
2 MafumuNgakhale kuti
ambiri ankachita zoipa,ochepa anali okhulupirika
KHALANI BWENZI LA YEHOVA � ZOCHITA
s
PINDANI
PINDANI
www.jw.org � 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of PennsylvaniaTsamba 3
![Page 4: Lowezani Mabuku a M’Baibulo—Gawo 1 · Ezara Anathandiza kuti anthu ayambenso kulambiraYehova Nehemiya Anathandiza kuti mzinda ndi mpanda wake zimangidwenso KHALANI BWENZI LAYEHOVA](https://reader036.vdocuments.pub/reader036/viewer/2022071010/5fc85387fa69e7034b5c44c9/html5/thumbnails/4.jpg)
1 MbiriAnaphunzirapo kathu
pa zochitika zakale
2 MbiriMtunduwo unakumana ndi mavuto
chifukwa cha mafumu oipa.
EzaraAnathandiza kuti anthu
ayambenso kulambira Yehova
NehemiyaAnathandiza kuti mzinda
ndi mpanda wake zimangidwenso
KHALANI BWENZI LA YEHOVA � ZOCHITA
s
PINDANI
PINDANI
www.jw.org � 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of PennsylvaniaTsamba 4
![Page 5: Lowezani Mabuku a M’Baibulo—Gawo 1 · Ezara Anathandiza kuti anthu ayambenso kulambiraYehova Nehemiya Anathandiza kuti mzinda ndi mpanda wake zimangidwenso KHALANI BWENZI LAYEHOVA](https://reader036.vdocuments.pub/reader036/viewer/2022071010/5fc85387fa69e7034b5c44c9/html5/thumbnails/5.jpg)
EsitereAnayankhula molimba mtima
pa nthawi yoyenera
YobuKukhala wokhulupirika
kumasangalatsa Mulungu
MasalimoNyimbo zotamanda
chikondi cha Mulungu ndimphamvu zake
MiyamboNzeru zopezeka m’mawu ake
n’zothandiza kwambiri
KHALANI BWENZI LA YEHOVA � ZOCHITA
s
PINDANI
PINDANI
www.jw.org � 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of PennsylvaniaTsamba 5
![Page 6: Lowezani Mabuku a M’Baibulo—Gawo 1 · Ezara Anathandiza kuti anthu ayambenso kulambiraYehova Nehemiya Anathandiza kuti mzinda ndi mpanda wake zimangidwenso KHALANI BWENZI LAYEHOVA](https://reader036.vdocuments.pub/reader036/viewer/2022071010/5fc85387fa69e7034b5c44c9/html5/thumbnails/6.jpg)
MlalikiKutumikira Mulungu
n’kosangalatsa kwambiri
Nyimbo ya SolomoChikondi chenicheni
chimakhalapo nthawi zonse
YesayaMmene moyo udzakhalire
Yesu akadzayamba kulamulira
KHALANI BWENZI LA YEHOVA � ZOCHITA
s
PINDANI
PINDANI
www.jw.org � 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of PennsylvaniaTsamba 6