matenda a kolera - the compass for sbc

16
MATENDA A KOLERA zinyalala ndipo

Upload: others

Post on 11-Apr-2022

3 views

Category:

Documents


0 download

TRANSCRIPT

Page 1: MATENDA A KOLERA - The Compass for SBC

MATENDA A KOLERA

zinyalala ndipo

Page 2: MATENDA A KOLERA - The Compass for SBC
Page 3: MATENDA A KOLERA - The Compass for SBC

Funso: Kodi njira yolelera yoyamwitsa ndi yotani?

Kodi njira yolerera yoyamwitsa imagwira ntchito bwanji?

Kodi ndani angagwiritse ntchito njirayi?

Kodi ndani amene sakuyenera kugwiritsa ntchito njira yolerera yoyamwitsa?

Njira yolelera yoyamwitsa ndi njira yachilengedwe imene imagwira ntchito poyamwitsa mwakathithi pamene mwana asanakwane miyezi isanu ndi umodzi komanso mayi sanamusambire. Mayi atha kugwiritsa ntchito njira iyi atangobereka kufikira miyezi isanu ndi umodzi.

Imalepheretsa mazira amayi kukhwima kotero mayi sangatenge mimba. Njira iyi ndiyodalirika chifukwa mwa amayi 100 amene akugwiritsa ntchito njirayi, amayi 98 sangatenge mimba

Njirayi atha kugwiritsa ntchito ndi mayi wina aliyense amene akukwaniritsa zinthu zitatu izi:1. Mayi amene sanamusambire mwana 2. Mwana akhale akuyamwa bere

pafupipafupi usana ndi usiku (mwakathithi) kosachepera kasanu ndi katatu, komanso sakudya kapena kumwa zakumwa zina koma bele lokha.

3. Mwana akhale wochepera miyezi isanu ndi umodzi

1. Mayi amene amusambira mwana wake2. Mayi amene mwana wake wayamba kudya

zakudya zina kapena sakuyamwa pafupipafupi

3. Mayi amene mwana wake wakwanitsa miyezi isanu ndi umodzi yakubadwa

Kodi ubwino wanjira yolerera yoyamwitsayi ndi wotani?

A) ubwino kwa amayi

B) ubwino kwa mwana

l Imathandiza kuti chiberekero chibwerere mmalo mwake mwamsanga ndipo imachepetsa kutaya magazi

l Imachepetsa matenda akusowa kwa magazi mthupi

l Mayi atha kuyamba kugwiritsa ntchito njirayi atangobereka

l Palibe zotsatira zovuta pamene mayi akugwiritsa ntchito njirayi

l Njirayi imalimbikitsa chikondi pakati pa mayi ndi mwana

l Ndi njira yachilengedwe imene sisowa kugwiritsa ntchito zipangizo kapena mankhwala.

l Banja limakhala ndi nthawi yoganizira ndikusankha njira zina zolerera pamene njirayi isanasiye kugwira ntchito

l Imalimbikitsa mayi kuyamwitsa mwana mkaka wamawere nthawi zonse.

l Njirayi siisokoneza mayi ndi bambo kugonana.

l Imapereka chitetezo kumatenda osiyanasiyana monga chikuku

l Mkaka wammawere muli chakudya chokwanira ndi choyenera kwamwana kwa miyezi isanu ndi umodzi yoyambirira.

l Kuyamwitsa kumateteza mwana kumatenda monga otsegula, mphenga (kutuluka mafinya mkhutu) ndi ena otero.

21 3

Page 4: MATENDA A KOLERA - The Compass for SBC

Njirayi imalimbikitsa chikondi pakati pa mwana ndi mayi

1. Ndi njira yolerera ya nthawi yochepa {miyezi isanu ndi umodzi (6)}

2. Siyodalirika pokhapokha mfundo zitatu zomuyenereza mayi zitakwaniritsidwa:- Mayi sanasambire mwana wake- Mwana wake sanayambe kudya zakudya

zina- Mwana wake sanapitirire miyezi isanu

ndi umodzi (6) yakubadwa3. Siteteza kumatenda opatsirana pogonana

kuphatikizapo HIV4. Ngati mayi ali ndi HIV, pali chiopsezo choti

atha kumpatsira mwana kudzera mumkaka wammawere

1. Njira yolerera yoyamwitsa imagwira ntchito ngati zinthu zitatu izi zakwaniritsidwa: - Mayi sanasambire mwana wake- Mwana wake sanayambe kudya zakudya

zina- Mwana wake sanapitirire miyezi isanu

ndi umodzi yakubadwa2. Yambani kugwiritsa njira ina yolerera ngati

chimodzi mwa zinthu zitatu tatchulazi sizinakwaniritsidwe

3. Pitirizani kuyamwitsa ngakhale mukugwiritsa ntchito njira zina zolerera

4. Yamwitsani mwana wanu kufikira ali ndi zaka ziwiri zobadwa ngati palibe vuto liri lonse

5. Pali njira zina zambiri zolerera zimene sizisokoneza kuyamwitsa mwana

Ngati mukufuna kudziwa zambiri kaonaneni ndi alangizi azakulera mdera lanu kapena pitani kuchipatala chimene muli nacho pafupi

Kuyipa kwake kwa njira yolerera yoyamwitsa

Kumbukirani izi

. Originally produced by Health Education Unit in collaboration with MCHIP

Njirayolerera

yoyamwitsa

Page 5: MATENDA A KOLERA - The Compass for SBC

Uthengawu walembedwa ndi unduna wa zaumoyo ndi chithandizo chochokera ku bungwe la United States Agency for International Development (USAID) kudzera mu pulojekiti ya SSDI.

Page 6: MATENDA A KOLERA - The Compass for SBC

1 5

73 4

6

8

Mwangolandira kumene masikito anuo khala ndi mankhwala opha udzudzu kwa nthawi yaitali kuti banja lanu litetezedwe ku Malungo.

Pisilani masikito anu pansi pa mphasa kapena matilesi kuti udzudzu usapeze mpata olowa mkati mwa masikito.

Musanayambe kugwiritsa ntchito masikitowa, apachikeni kuti apitidwe mphepo.

M’mawa kukacha, kulungani masikito anu m’mwamba kuti asaonongeke kapena kuda. Izi zimathandizanso kuti mchipinda mwanu mukhale motakasuka.

Mukachapa masikito anu, ayanikeni moyala pansi pa mthunzi.

Musachape masikito anu koposera katatu pa chaka.

Malungo ndi matenda oopsa. Choncho, usiku uliwonse kwa chaka chonse, gonani m’masikito onyikidwa m’mankhwala ophau dzudzu kwa nthawi yaitali.

Kenaka apachikeni pa malo ogona.

2

Page 7: MATENDA A KOLERA - The Compass for SBC

Masikito amateteza inu ndi banja lanu ku malungo. Kumbukirani kuti kuchiza malungo ndi kotaitsa nthawi ndi chuma. Kulibwino kupewa.

Ubwino wa masikito umakhala wopambana pa banja komanso pa mudzi ngati aliyense akugona m’masikitowa.

Ana amene amadwaladwala malungo sangachite bwino mkalasi. Makolo amene amadwaladwala malungo sakhala ndi mpata wabwino wotukula ma banja awo.

Mudzi womwe uli ndi anthu osadwaladwala malungo umakhala ndi anthu ambiri omwe amatha kugwira ntchito zachitukuto.

MasikitoNdi a Mtengo

Wapatali

TIPINDULA NGATITONSE TIKUGONAM’MASIKITO

Page 8: MATENDA A KOLERA - The Compass for SBC

Kugulitsa masikito kwa asodzi kumalepheretsa ena kugona m’masikitowa. Izi zimabwezeretsa m’mbuyo ntchito yogonjetsa malungo pa banja komanso pa mudzi.

Kholo la udindo siligulitsa masikito ndipo ngati ena akuchita izi, limakanena kwa mafumu, alangizi a zaumoyo, mabungwe komanso ofesi yoteteza nsomba.

Kugwiritsa ntchito masikito pa usodzi ndi kuphwanyamalamulo a boma.

Msodzi waudindo amateteza mudzi wake ku imfa za malungo. Samagwiritsa ntchito masikito ndipo amakanena kwa mafumu komanso ku ofesi yoteteza nsomba ngati ena akukakamira kuchita izi.

Masikito ali ndi mabowo ang’onoang’ono omwe amagwira ana a nsomba. Kuti titeteze nsombazi, tikuyenera kugwiritsa ntchito ma neti ovomerezeka osati masikito. Nsomba zikachulukana, mabanja athu angathe kukhala a thanzi.

Malawi GovernmentMinistry of Health

Ululani umbava wa maneti ndi mankhwala poimba 847 (TNM/AIRTEL/ACCESS) kapena 80000847 (MTL)

Mfumu yozindikira imakhazikitsa malamulo oletsa anthu kugwiritsa ntchito masikito pa usodzi ndipo siichita katangale.

Tikhoza kupindula ngati tonse tikugona m’masikitowa. Tikhoza kukhala ndi:• Ana osajomba ku sukulu chifukwa cha malungo.• Makolo okhala ndi nthawi yotukula mabanja awo.• Mudzi wa chitukuko.

Mu kabukuka muli mauthenga ofunikira kwambiri pa umoyo wa inu ndi anthu ena mdera lanu. Chonde bwerekani anzanu kuti awerengeko kapena agayireni mauthenga omwe ali mu kabukuka.

Page 9: MATENDA A KOLERA - The Compass for SBC

masikikitiot.oN.sNos-mobmazbiataczhiutalu-ckhaunalu,mkabnbaan-jmjaaabanja atnhtu-haunganthgeaktuhke-hakluakahnathlanazi.nt

We Value

Our Net

IF EVERYONE SLEEPS UNDER A MOSQUITO NET, EVERYONE WILL BENEFIT.

Villages with few or no malaria cases are productive and the people are healthy and able to participate in development activities.

Children who frequently su�er from malaria cannot perform well in school. Parents who frequently su�er from malaria cannot be as productive as those who are healthy.

Treated nets work well when everyone in the community sleeps under the net. This is because the treated mosquito net kills mosquitoes that transmit malaria

Long Lasting Insecticide Treated Nets protect your family and community from malaria.Remember that treating malaria is more expensive than preventing it.

Page 10: MATENDA A KOLERA - The Compass for SBC

A responsible chief will form by-laws that punish culprits and will resist bribes.

When everyone sleeps under a treated net in our community, all of us will benefit. we can have:

• Children who are not absent from school.• Parents who provide for their families.• Chief with healthy subjects.

Malawi GovernmentMinistry of Health

To report theft of mosquito nets and medicines, you can also call 847 (TNM/AIRTEL/ACCESS) and 80000847 (MTL)

This leaflet contains important messages for you, your family and your community. Please share the leaflet or information contained in it with others

A responsible fisherman does not use the mosquito net for fishing. He reports culprits to the chief and the Fisheries Department.

A responsible parent resists any attempts to sell a mosquito net for fishing and will report culprits to the chief, the health worker or the Fisheries Department.

Selling treated nets to fishermen prevents someone from sleeping under a net. This defeats our communal fight against malaria.

A mosquito net has small holes and it catches baby fish. By not using mosquito nets for fishing, we will protect the baby fish and have more fish in future. More fish means better nutrition for our families.

It is illegal to fish using mosquito nets.

Page 11: MATENDA A KOLERA - The Compass for SBC

Vision: Hope to those in need

Mission: To alleviate human suffering and improve the quality of life of vulnerable people through

relief, development activities and dissemination of the movement’s fundamental principles.

Our mandate: To provide relief and aid to people affected by conflict and disasters.

Kodi njira za kulera zokhalitsa ndingazipeze kuti?

• Njirazizimapezekamzipatalazamderalanu• Funsaniazachipatalakutiakudziwitsenikomwe

mungapezenjirazimwamsanga

ThismessageisbroughttoyoubytheMinistryofHealthwithsupportfromtheUnitedStatesAgencyforInternational

Development(USAID)throughtheSSDI-CommunicationProject.Kuyankha mafunso ndi nkhawa zanu zonse

Njira zonse za kulera zokhalitsa ndi zovomelezeka ndi Unduna wa za Umoyo. Ngati muli ndi mafunso kafunseni alangizia za umoyo mdera lanu

Banjalaling’onosilivutakusamalira.Khalanindibanjalathanzi.Khalanindibanjalaling’no.

Njira zakulera zokhalitsa

Njirazi sizimateteza munthu ku matenda opatsirana pogonana

FAMILY PLANNING METHODS LEAFLET 4.indd 1 4/5/14 9:17 AM

Page 12: MATENDA A KOLERA - The Compass for SBC

Kodi njira za kulera zokhalitsa ndi chiyani ?Izi ndi njira za kulera zomwe zimathandiza kupewa kutengamimba yosakonzekera kwa nthawi yaitali kuyambira zakazitatumpakanazakakhumimukayigwiritsantchitokamodzi.Mayiathakusiyakugwiritsanjirazindikuyambansokuberekanthawiiliyonseyomweangafunekutero

Nanga njira za kulera zokhalitsa zomwe zimapezeka ku Malawi kuno ndi ziti?1.IMPULANTI:Njirayaimpulantinditimapulasitikitatin’gonoting’onokwambiritomwetimaikidwamkatimwakhungulapamkonondipoimathandizakutimayialekekusambamasikuakeakakwanachonchosangatengemimba.

2.Lupu:Njirayiimaikidwamkatimwachiberekerondipoimalepheretsamphamvuyaabambokulowamchiberekeromondikuperekamimba

Kodi ndingayambenso kubereka nditasiya kugwiritsa ntchito njira za kulera yokhalitsa?• Inde,njirazakulerayokhalitsaithakuchotsedwanthawi

iliyonsendipoinumuthakutengamimbapasanapitenthawiyaitali.

• Amayienaakhozakukhalamiyeziingapoasanayambekusambangatim’meneamachitirakale.

Kodi njira za kulera zokhalitsa ndizosaopsa kwa mayi?• Njirazizidayesedwam’maikoambiripadzikolapansindipo

undunawazaumoyoudazivomerezansokutindizodalirika.• Njirazisizibweretsamavutoaliwonseokhudzamimba,mwana

omuyembekezerakapenamatendaaliwonse.Siziyambitsansomavutoaliwonseoterem’tsogolo.

Kugwiritsa ntchito kamodzi kokha, kutetezedwa kwa nthawi yaitali

Nanga ubwino wa njira za kulera zokhalitsa ndi wotani?1. Ndizosavutakugwiritsantchito:Mukangoikitsakamodzi

mwathananazo.Simufunikansokuchitachinachilichonsekutinjiraziipitilirekugwirantchito.

2. Simupitapitakuchipatalakukatenganjirazakulera.3. Simungaiwalekugwiritsantchitonjirazichifukwa

zimaikidwakamodzibasi;kusiyanandinjirazinamongamapilitsi,makondomundijakisonizomwemumagwiritsantchitonthawindinthawi.

4. Njirazomwezimaikidwam’chiberekero(lupu)zimathandizansokuchepetsamatendaenaakhansayam’chiberekero.

Kodi ndingathe kuyamba kugwiritsa ntchito njira yolerera yokhalitsa nditangobereka kumene kapena nditapita padera?• N’kothekakutengansomimbautangoberekakumenekapena

kupitapadera.• Funsaniachipatalakutiakufotokozerenizanjirazakulera

zokhalitsazokuyeneranizomwemungayambekugwiritsantchitopatangopitamasikuawiriokhakuchokeratsikulobereka.

Njirazi sizibweretsa chiopsezo pa thupi komanso nzodalilika

Kodi njira za kulera zokhalitsa sizibweretsa mavuto pa nkhani yogonana?• Njirayalupusiyisokonezapogonanandiposipweteka.• Njirayaimpulantindinjirazinazonsezokhalitsasizisintha

chilakolakochogonanakomansom’menemumamveramukamagonana.

Kodi pali mavuto aliwonse omwe amabwera pa thupi chifukwa chogwritsa ntchito njira za kulera zokhalitsa• Amayienaathakuonakusinthikakwinam’thupilawokwa

nthawiyochepaakatenganjirazichifukwachosazolowerakomanjirazisizibweretsamavutooopsakwamayi.

• Funsaniachipatalakutimudziwezambirizaizipanthawiyomwemukufunakusankhanjirayakulera.

• Pitanikuchipatalangatimungaonekusinthakwinakulikonsepanthawiyomwemwayambakugwiritsanjirazakulerazokhalitsa

Nanga ndi ndani angagwiritse ntchito njira za kulera zokhalitsa? • Amayionseomweanafikamsinkhuwobereka• Amayiomweakuyamwitsakapenasiakuyamwitsa• Amayi omwe ali ndi HIV ngakhale omwe akumwama ARV.

Ngati muli ndi HIV, ndi koyenera kugwiritsa ntchito njirazimophatikizandinjirayamakondomu.

FAMILY PLANNING METHODS LEAFLET 4.indd 2 4/5/14 9:18 AM

Page 13: MATENDA A KOLERA - The Compass for SBC

Kugona mu netiTigone mu neti yonyikidwa m’makhwala opha udzudzu usiku uliwonse kwachaka chonse ngakhale sitikuona kapena kumva kulira kwa udzudzu.

Kupopela mankhwala mnyumbaNgati nyumba yathu inapoperedwa mankhwala opha udzudzu, tipitirizebe kugona mu neti kuti tionjezere chitetezo chathu ku matenda a malungo.

2

Kumwa mankhwala a SPNgati tili woyembekezera timwe mankhwala a SP kosachepera katatu kuti tidziteteze ku malungo.

3

Kupita ku chipatala msangaNgati tadwala litsipa kapena tikumva kuphwanya mthupi tipite ku chipatala pasanathe tsiku kuti akatiyeze ngati tili ndi malungo ndi kulandira mankhwala oyenera.

4

Kuyezetsa malungoTimwe mankhwala a malungo pokhapokha ngati tayezedwa ndi kupezekandi malungo.

5

Kumaliza mulingo wa mankhwala

Timalize kumwa mankhwala a malungo mwandondomeko kuti tichire ku matendawa.

6

1

Chipatala

Njira zisanu ndi imodzi (6) zomwetingatsate kuti tigonjetse malungo

Malawi GovernmentMinistry of Health

C

M

Y

CM

MY

CY

CMY

K

FLIER A5 ARTWORK.pdf 1 12/4/13 4:52 PM

Page 14: MATENDA A KOLERA - The Compass for SBC

Udzudzu woyambitsa malungo umapezeka chaka chonse: Nthawi ya mvula, yotentha komanso yozizira ngakhale nthawi zina sitiwuona kapena kuumva ukulira.

Maneti onyikidwa m’mankhwala opha udzudzu ndi abwino kwa aliyense. Alibe chiopsezo china chilichonse kwa ana, akulu ngakhalenso ziweto.

Mankhwala a SP alibe chiopsezo chilichonse kwa mayi woyembekezera. Mukhoza kumwa mankhwalawa kopitilira katatu pa nthawi yomwe mukuyembekezera.

Ngati mukumva litsipa kapena kuphwanya mthupi muyenera kuyezetsa malungo musanamwe mankhwala a malungo.

Kodi Mukudziwa?

Ngati muli ndi mafunso kafunseni mlangizi wa zaumoyo mdela lanu.

Dzitetezeni ku malungo.Tetezani banja lanu.

Tetezani mudzi wanu.Tetezani dziko lanu.

C

M

Y

CM

MY

CY

CMY

K

FLIER A5 ARTWORK.pdf 2 12/4/13 4:52 PM

Page 15: MATENDA A KOLERA - The Compass for SBC

6.0 Kupereka Zinki kwa mwana

Kwa mwana wa miyezi iwiri (2) mpakana isanu ndi umodzi (6):

• Mpatsenithekalam’buluwaZinkikamodzipatsiku.

• Muyamwitsenipafupipafupi.

Kwa mwana wa pakati pa miyezi isanu ndi umodzi (6) ndi zaka zisanu (5):

• Mpatsenim’buluumodziwathunthukamodzipatsiku.

• Pitirizanikumupatsazakudyazamadzimadzikomansozakumwa.

• Ngatialiwoyamwa,muyamwitsenipafupipafupi.

• Mulimbikitsenikudyazakudyazamagulusikisitsikulirilonse.

Tsatirani ndondomeko yakamwedwe ka zinki kuti mwana wanu atetezedwe ku matenda otsekula m’mimba kwa miyezi ina iwiri kapena itatu.

Pitani ndi mwana ku chipatala mwamsanga ngati:• Akutsekulabem’mimbapatathamasikuatatu

akumwaZinkindiORS.• Akuchitachimbudzichosakanikiranandi

magazi.• Akuwonekawofooka.• Akukanakudya,kumwakapenakuyamwa.

UthengawuwalembedwandiundunawazaumoyondichithandizochochokerakuUSAIDkudzerakupulojekitiyaSSDI

ORS ndi Zinki!

Mwanaakatsekulam’mimba...

Zimachiritsa msanga.

Ngakhalemwanawanuatachiramsanga,pitirizanikumupatsaZinkikwamasikukhumi(10)kutimupewematendaotsekulam’mimbakwamiyeziiwirikapenaitatuyotsatira.

Page 16: MATENDA A KOLERA - The Compass for SBC

4.0 Ubwino wa Zinki kwa mwana wotsekula m’mimbaKupatsamwanawanuZinkipamodzindiORSkumathandizamotere:

• Mwanaamalekakuchitachimbudzipafupipafupi.Izizimathandizakutiasafooke.

• Mwanaamachiramsanga.• Mwanaamakhalawotetezedwakumatenda

otsekulam’mimbakwamiyeziiwirikapenaitatuyotsatira.

• Mwanaamakhalandichilakolakochazakudyandipopoteroamapezamphamvukomansoamachiramsanga.

Ngati mwana akuchita chimbudzi cha madzimadzi koposera katatu patsiku pitani naye mwamsanga ku chipatala.

Zinki akupezeka m’zipatala zonse m’dziko muno. Muthanso kugula Zinki ku sitolo kapena m’malo ogulitsira mankhwala.

1.0 Kutsekula m’mimbaMwanaakamatsekulam’mimbaamatayatimicheretam’thupi.UmodzimwatimicheretindiZinkiyemweamathandizamwanakukhalandithanzi.Matendaotsekulam’mimbaamaphaanaambirimunom’Malawi.KomankhaniyabwinondiyakutimuthakupulumutsamoyowamwanawanupogwiritsantchitoORSndiZinki.

2.0 Kuzindikira matenda otsekula m’mimbaNgatimwanaakuchitachimbudzichamadzimadzikokwanirakatatupatsiku,ndiyekutimwanayowatsekulam’mimba.

3.0 Kodi tichite chiyani mwana akatsekula m’mimba?Mwanaakangoyambakutsekulam’mimba,mpatseniORSndiZinki.DziwanikutikumwetsamwanaORSndinjirayodalirikayobwezeretsamadzindimphamvum’thupi.Zinkiamathandizirakutsekam’mimba.

Zinki amathandiza kuti mwana achire msanga.

5.0 Ubwino wina wa ZinkiZinkindiwofunikiransomunjiraizi:

• Amathandizamwanakukhalawathanzikomansowanzeru.

• Amathandizakulimbikitsachitetezochamwanapopewamatenda.

M’bulu wa Zinki umasungunukam’madzi

2

4

13