lowezani mabuku a m’baibulo—gawo 1 · ezara anathandiza kuti anthu ayambenso kulambirayehova...

Post on 20-Aug-2020

2 Views

Category:

Documents

0 Downloads

Preview:

Click to see full reader

TRANSCRIPT

Lowezani Mabuku a M’Baibulo—Gawo 1Dulani makadiwa kuti akuthandizeni kuloweza mabuku ena a m’Baibulo a Malemba aChiheberi. Funsani anthu a m’banja mwanu komanso anzanu.

GenesisBuku lofotokoza

mmene paradaiso anathera

EkisodoMulungu anapulumutsaanthu ake modabwitsa

LevitikoMalamulo a Mulungu

anawathandiza kukhalaoyera tsiku lililonse

NumeriEna analephera kukalowa

m’Dziko Lolonjezedwa

KHALANI BWENZI LA YEHOVA � ZOCHITA

s

PINDANI

PINDANI

www.jw.org � 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of PennsylvaniaTsamba 1

DeuteronomoAnalimbikitsidwa

kuti akhale omvera

YoswaBanja lililonse

linali ndi malo awoawo

OweruzaAnthu a Mulungu

ankachita zinthu zodabwitsa

RuteAnapeza mwamunandiponso pokhala

KHALANI BWENZI LA YEHOVA � ZOCHITA

s

PINDANI

PINDANI

www.jw.org � 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of PennsylvaniaTsamba 2

1 SamueliMulungu anasankha

Davide kuti akhale mfumu

2 SamueliM’banja lake munali mavutochifukwa cha machimo ake

1 MafumuUfumu unagawanika,

wina kumpoto wina kumwera

2 MafumuNgakhale kuti

ambiri ankachita zoipa,ochepa anali okhulupirika

KHALANI BWENZI LA YEHOVA � ZOCHITA

s

PINDANI

PINDANI

www.jw.org � 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of PennsylvaniaTsamba 3

1 MbiriAnaphunzirapo kathu

pa zochitika zakale

2 MbiriMtunduwo unakumana ndi mavuto

chifukwa cha mafumu oipa.

EzaraAnathandiza kuti anthu

ayambenso kulambira Yehova

NehemiyaAnathandiza kuti mzinda

ndi mpanda wake zimangidwenso

KHALANI BWENZI LA YEHOVA � ZOCHITA

s

PINDANI

PINDANI

www.jw.org � 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of PennsylvaniaTsamba 4

EsitereAnayankhula molimba mtima

pa nthawi yoyenera

YobuKukhala wokhulupirika

kumasangalatsa Mulungu

MasalimoNyimbo zotamanda

chikondi cha Mulungu ndimphamvu zake

MiyamboNzeru zopezeka m’mawu ake

n’zothandiza kwambiri

KHALANI BWENZI LA YEHOVA � ZOCHITA

s

PINDANI

PINDANI

www.jw.org � 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of PennsylvaniaTsamba 5

MlalikiKutumikira Mulungu

n’kosangalatsa kwambiri

Nyimbo ya SolomoChikondi chenicheni

chimakhalapo nthawi zonse

YesayaMmene moyo udzakhalire

Yesu akadzayamba kulamulira

KHALANI BWENZI LA YEHOVA � ZOCHITA

s

PINDANI

PINDANI

www.jw.org � 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of PennsylvaniaTsamba 6

top related